Usalire" is a song done by Noel M Christian. This guy is so hottest in teams of gospel music. There is a hope that Christian is going to shake Malawi with his gospel music. He have so beautiful angels voice so that when he is singing you can feel holy spirit inside of you. Here is the comment from himself.


NOEL: I love gospel music a lot and I know I have a work I suppose to do in music. I believe that my music is special ministry I'm going to do which God gave me. That is why I have a group and I call it "MUSIC MINISTRY🎧". So please be with me and let us walk together with gospel music.


VORTNET: That was a spech from Noel. Now he have a project whereby he is doing his EP called AVITAND. Please help this guy to do his amazing music. You can follow him on Facebook page NOEL M Christian.

God bless you for your understanding.❤

Noel m Christian,
Mwana wa Mtasambala aaaooo it's me.

Veci 1
Mwadwala mwapita kuchipatara,
Akuuzani a Dokotala,
Kut matenda omwe mwadwalawo,
Simmungathe kuchilaso,


Mwataya chiyembekezo chani,
Mzimu wanu walefuka ndi matha,
Mwataya zanu zanse,
Mwaluza achikondi.

Chorus

Hoooo koma iwe!!!

Usalire,
Usalire
Usalire,
Usalire

Hayi usalire no!
Usalire,
Usalire,
Usalire,
Usalire.

Veci 2

Msanamira ya moyo wanu yantchwoka,
Muli mndende koma simnalakwe,
Aaaaaakumangani koma simnalakweeee!

Ngati misona ya mingo,
Kulira pamwamba pa phiri,
Ana inu mukuvutika koma palibe ukuthandizani musalire!!

Chorus

Hooo koma iwe !!!!

Usalire,
Usalire,
Usalire,
Usalire.

Hayi usalire!!
Usalire,
Usalire,
Usalire,
Usalire,

Bending

Musalire no,
Ndimene moyo umayendala,
Komano tiyeni tilimbike kupephera,

Popeza golide,
Sangakhale golide,
Asanadutse mng'ango ya moto,
Nyengo zimenezi zikulimbitsa.

Chorus.

Hoo iwe !!!

Usalire,
Usalire,
Usalire,
Usalire,

Hayi usalire!!!
Usalire,
Usalire,
Usalire.

0 نظرات
    نظری یافت نشد

:: / ::
::
/ ::

صف