Nyimboyi ndiyoimbidwa ndi Noel M Christian yomwe ikufotokoza zammene anthu amakhalira osasamala akakhala ndi zithu. Katswiri oimbayu akugwilitsira liwu lotchedwa "#ADZAGUNDAMGOLO" lomwe likutathauza pachizungu #"regret" pofuna kuwasonyezera ovela kuti adzalira kapena adzalanguluka akaseweletsa mwayi omwe ali nawo. Nyimboyi ukuchokera my E.P yotchedwa AVITAND. Chonde like the song and share.

Adzagunda mgolo.

0 הערות
    לא נמצאו הערות

:: / ::
::
/ ::

תוֹר