Iyi ndi nyimbo yomwe ikufotokoza zambiri zokhudza kusasamala kwa anthu pa moyo wao wa tsiku ndi tsiku. Makamaka ili ndi uthenga ochenjeza, ophuzitsa, olimbikitsa. Chonde kwaine monga Noel
ndikanakonda kuti uthenga omwe nyimboyi ya nyamula ugwilitsidwe ntchito pa moyo omwe timakhala. Please like and share this song. If posible encourage me .
Help me by buying this song online

Adzagunda mgolo.

0 نظرات
    نظری یافت نشد

:: / ::
::
/ ::

صف